bestellen

home | boeken | pers | agenda

boekingen
prozagedichten
foto's
bestellen
contactprose poems

nederlands | english | español
deutsch | frysk |
chichewa

 

 Bambo wa njinga ya moto* (Motorman)


Amakonda kuzungulira ndi njinga yake ya moto, ine sindimadziwa kuti chikunchitikira nchiyani mímaganizo ake.

Tsiku lina ndina mutsatira kukanyumba yake ku Míkhalango.

Ndinayenda mpaka pakanyumbapo ndikukakha, chitseko chake nkutsekula.

Nditatsekula ndinawona míbambo wa njinga yamoto uja atagona chafufumimba pamitengo pansi.

Anadzidzimuka ndikuyimilira akundi yaníganitsitsa mwachidwi ndi nkhope yodabwa.

Ndinkafuna kulankhula naye koma ndisanatelo bambo wa njinga ya motoyo anasowa osabwerelanso.

Ndinalowa mínyumbamo momwe ndinakhazikika kwa zaka makumi awiri.

Mawuwa ndiwowonadi: Nyumba yatsopano ndiyabwino kusiyana ndiyakale.

Translation: Tosh Malunga, Senga Bay

* Chichewa is the main language of Malawi. 'Bambo wa njinga ya moto' literally means 'Man with bike of fire' / 'Man met fiets van vuur'.


>>Klik hier voor het radioverhaal dat Nyk maakte voor het Vpro-programma Cantina over zijn verblijf in Malawi.


©nykdevries 2010